Translations by Herald Luwizghie

Herald Luwizghie has submitted the following strings to this translation. Contributions are visually coded: currently used translations, unreviewed suggestions, rejected suggestions.

135 of 35 results
~
Thank you for choosing Ubuntu 14.04. This version brings some exciting changes including a totally redesigned desktop interface, Unity. While Ubuntu is configured, this slideshow will show you around.
2015-03-04
Zikomo kwambiri posnkha Ubuntu 14.04. Mtundu uwu ukubweletselani zosangalatsa zatsopano kuonjezelapo maonekedwe atsopano, ndi mgwilizano. Podikila Ubuntu akukhonzedwa, zithunzi zikudza apazi zikuonetsani m'mene mungathe kupeza zina ndi zina.
~
Welcome
2015-02-27
Mwalandilidwa
~
I'm installing #Ubuntu!
2015-02-27
Ndiku khazikitsa #Ubuntu!
~
Let’s talk Ubuntu
2015-02-27
Tiyeni tiyankhule Ubuntu
1.
Access for everyone
2015-02-27
Kuvomeleza aliyense
2.
At the heart of the Ubuntu philosophy is the belief that computing is for everyone. With advanced accessibility tools and options to change language, colour scheme and text size, Ubuntu makes computing easy – whoever and wherever you are.
2015-02-27
Pamtima wa Ubuntu palichikhulupiliro chokuti Komputa ndiya aliyense. Podzela mpata wakutha kusankha chiyankhulo, mtundu komanso kakulidwe kamalemba, Ubuntu imapangitsa ntchito za komputa kuphweka - Aliyense kuli konse komwe muli.
3.
Customization options
2015-02-27
Mipata yakusintha maonekedwe
4.
Appearance
2015-02-27
Maonekedwe
5.
Assistive technologies
2015-03-02
Umisili wa chithandizo
6.
Language support
2015-02-27
Chithandizo pa chiyankhulo
7.
Make the most of the web
2015-03-04
Kugwilitsa ntchito intaneti.
8.
Ubuntu includes Firefox, the web browser used by millions of people around the world. And web applications you use frequently (like Facebook or Gmail, for example) can be pinned to your desktop for faster access, just like apps on your computer.
2015-03-02
Ubuntu amabwela ndi Firefox, bulawuza yomwe anthu zikwi amagwilitsa ntchito dziko lonse lapansi. Komanso mapologalamu ena omwe mungathe kugwilitsa ntchito zapa intaneti pafupi pafupi (monga Facebook kapena Gmail, mwa chitsanzo) mutha ku dinda kapena kutsindikiza pa mwamba pa komputa yanu kuti mudzigwilitsa ntchito mwachangu, monga zikhalila ndi mapologalamu ena mukomputa mwanu.
9.
Included software
2015-03-02
Mapologalamu oyendetsela komputa amwe awonjezeledzwa.
10.
Firefox web browser
2015-03-02
Firefox pulauza wa intaneti
11.
Supported software
2015-02-27
Ma Software amwe alindi chithandizo
12.
Flash
2015-02-27
Flash
13.
Chromium
2015-02-27
Chromium
14.
Any questions?
2015-02-27
Pali funso lina?
15.
Check out <a href="http://askubuntu.com/">askubuntu.com</a> for answers to all your Ubuntu questions. There’s a good chance your question will have been answered already and, if not, you’ll find thousands of volunteers eager to help. For more support options, go to <a href="http://www.ubuntu.com/support">ubuntu.com/support</a>.
2015-03-02
Onani izi <a href="http://askubuntu.com/">askubuntu.com</a> kuti mupeza mayankho kumafunso onse okhudza Ubuntu. Mwina palimwayi wokuti funso lanu linayankhidzwapo kale, ngati sichoncho, mupesa anthu mazana mazana odzipeleka kukuthandizani. Kuti mupeze chithandizo china, pitani ku <a href="http://www.ubuntu.com/support">ubuntu.com/support</a>.
16.
Take your music with you
2015-02-27
Tengani nyimbo muyende nazo
17.
Ubuntu comes with the amazing Rhythmbox music player. With advanced playback options, it's simple to queue up the perfect songs. And it works great with CDs and portable music players, so you can enjoy all your music wherever you go.
2015-03-04
Ubuntu amadza ndi Rhythmbox pologalamu yosewelela nyimbo. Ndimwayi wakasankhidwe kamasewelede anyimbo, yosavuta kasanjidwe kanyimbo zanu. Amagwilanso bwino ntchito ndi ma CD ndi timawailesi tam'manja tosewelela nyimbo, kuti muthe kunjoya nyimbo zanu zonse konse mukupita.
18.
Rhythmbox Music Player
2015-03-04
Rhythmbox pologalamu yosewelela nyimbo
2015-02-27
Rythmbox posewelela nyimbo
19.
Everything you need for the office
2015-02-27
Chilichonse mungachifune mu ofesi
20.
LibreOffice is a free office suite packed with everything you need to create documents, spreadsheets and presentations. Compatible with Microsoft Office file formats, it gives you all the features you need, without the price tag.
2015-03-04
LibreOffice ndi gulu lamapologalamu otimutha kugwilitsa ntchito mu Office a ulele omwe mutha kupangila makalata, zokhudza kuwelengela ndinso zothandizila kuonetsera nthcito yanu. Umagwilizana ndi mtundu wama failo a Microsoft Office, umakupatsani zonse zofunikila pagwilitsa ntchito mapologalamu awa popanda ndalama iliyonse.
21.
LibreOffice Writer
2015-02-27
LibreOffice Writer
22.
LibreOffice Calc
2015-02-27
LibreOffice Cal
23.
LibreOffice Impress
2015-02-27
LibreOffice Impress
24.
Have fun with your photos
2015-02-27
Sangalani ndi zithunzi zanu
25.
Shotwell is a handy photo manager that is ready for your gadgets. Connect a camera or a phone to transfer your photos, then it’s easy to share them and keep them safe. If you’re feeling creative, you can try lots of photo apps from the Ubuntu Software Center.
2015-03-04
Shotwell ndi pologalamu yaing'ono yothandizila kuzithunzi zanu. Lumikizani lamya yanu kapena chojambulila chanu, ndipo ndiposavuta kuti mu sunge kapena kugawana ndi azinzanu zithunzizi. Ngati mulindiluso mutha kuyesanso mapologalamu ena ambili omwe mutha kugwilitsa ntchito pazithunzi zanu kudzela ku Ubuntu Software Center.
26.
Shotwell Photo Manager
2015-02-27
Shotwell photo Manager
27.
GIMP Image Editor
2015-02-27
GIMP kosinthila zithunzi
28.
Pitivi Video Editor
2015-02-27
Pitivi kosinthila canema
29.
Find even more software
2015-02-27
Pezani ma software ena ambiri
30.
Say goodbye to searching the web for new software. With Ubuntu Software Center, you can find and install new apps with ease. Just type in what you’re looking for, or explore categories such as Science, Education and Games, alongside helpful reviews from other users.
2015-03-04
Tsanzikanani ndiku yang'ana mapologalamu atsopano podzela ku Intaneti, Pogwilitsa ntchito Ubuntu Software Center, mutha kupeza ndikukhazikitsa mapologalamu atsopano mosavuta. Mwachtsanzo, lembani dzina lapologalamu yomwe mukufuna, kapena yang'anani pomagulu amapologalamu monga Sayansi, Zamaphunziro ngi masewelo; komanso ndi maganizo aanzanu papologalamu mwasankhayo.