Translations by Herald Luwizghie
Herald Luwizghie has submitted the following strings to this translation. Contributions are visually coded: currently used translations, unreviewed suggestions, rejected suggestions.
150 of 111 results
1.
Connecting...
2015-02-26
Kulumikiza...
2.
Connection failed.
2015-02-26
Kulumikiza kwalepheleka
3.
Connected.
2015-02-26
Zalumikizana.
4.
Restart to Continue
2015-02-26
Yatsaninso kuti mupitilize
5.
Install
2015-02-26
Khazikitsani
6.
Install (OEM mode, for manufacturers only)
2015-02-26
Khazikitsani (gawo la OEM , la mafakitale okha)
7.
You are installing in system manufacturer mode. Please enter a unique name for this batch of systems. This name will be saved on the installed system and can be used to help with bug reports.
2015-02-26
Mukukhazikitsa makina awa mugawo la ku fakitale. Chonde lowetsani dzina lenileni la batch la makina awa. Dzinali lidza sungidwa mu sisitimu yo khazikidwa yi ndipo lidza thandiza popeleka malipoti ama vuto ena.
8.
You can try ${RELEASE} without making any changes to your computer, directly from this ${MEDIUM}.
2015-02-26
Mutha kuyesa ${RELEASE} popanda kusintha chilichonse muKomputa yanu podzela ku ${MEDIUM}
9.
Or if you're ready, you can install ${RELEASE} alongside (or instead of) your current operating system. This shouldn't take too long.
2015-02-27
Kapena ngati mwakhonzeka, mutha kukhazikitsa ${RELEASE} limodzi (kapena m'malo mwa) Operating system yomwe ilimo. Zimenezi sizikuyenela kutenga nthawi.
10.
Try ${RELEASE}
2015-02-27
Yesani ${RELEASE}
11.
Install ${RELEASE}
2015-02-27
Khazikitsani ${RELEASE}
12.
You may wish to read the release notes or update this installer.
2015-02-27
Muthakufuna kuwelenga izi release notes or update this installer
13.
You may wish to read the release notes.
2015-02-27
Muthakufuna kuwelenga izi release notes
14.
You may wish to update this installer.
2015-02-27
Muthakufuna ku update this installer
15.
Where are you?
2015-02-27
Mulikuti?
16.
Keyboard layout
2015-02-27
Kayalana kwa makiyi.
17.
Choose your keyboard layout:
2015-02-27
Sankhani kuyalana kwa makiyi.
18.
Type here to test your keyboard
2015-02-27
Lembani apa kuti muyese makiyi
19.
Detect Keyboard Layout
2015-02-27
Peza kayalidwe ka makiyi
20.
Detect Keyboard Layout...
2015-02-27
Peza kayalidwe ka makiyi...
21.
Please press one of the following keys:
2015-02-27
Chonde sindikizani limodzi mwa makiyi awa:
22.
Is the following key present on your keyboard?
2015-02-27
Kodi kiyi iyi ilipipo pa keyboard panu?
23.
Who are you?
2015-02-27
Ndiwe ndani?
37.
Your name:
2015-02-27
Dzina lanu:
38.
Your name
2015-02-27
Dzina lanu
39.
At least 8 characters password
2015-02-27
Liwu lachinsisi la malemba osachepela asanu ndi atutu
40.
Retype password
2015-02-27
Lembaninso liwu lachinsinsi
41.
Pick a username:
2015-02-27
Sankhani dzina lomwe mudzigwilitsa ntchito
42.
Username
2015-02-27
Dzina lomwe mudzigwilitsa ntchito
43.
2015-02-27
44.
Must start with a lower-case letter.
2015-02-27
Muyambe ndi lemba laling'ono.
45.
May only contain lower-case letters, digits, hyphens, and underscores.
2015-02-27
Mutha kulowetsa malemba aang'ono, manambala, chilumikizanitsa, ndi chilumikizanitso cham'musi zokha.
46.
Skip
2015-02-27
Dumphani
49.
Choose a password:
2015-02-27
Sankhani liwu lachinsisi
50.
2015-02-27
51.
Password
2015-02-27
Liwu la Chinsinsi
52.
Confirm password
2015-02-27
Tsimikizani liwu lachinsinsi
65.
Confirm your password:
2015-02-27
Tsimikizanu liwu lanu lachinsisi
66.
Your computer's name:
2015-02-27
Dzina la kompyuta yanu
67.
The name it uses when it talks to other computers.
2015-02-27
Dzina limene idzagwilitse ntchitopoyankhula ndi zinzake.
68.
Must be between 1 and 63 characters long.
2015-02-27
Likuyenela kutalika palati pa lemba limodzi ndi makumi asanu ndi limodzi ndi mphambu zitatu.
69.
May only contain letters, digits, hyphens, and dots.
2015-02-27
Mutha kukhala malemba, manambala, chilumikizanitso ndi mipumulo.
70.
May not start or end with a hyphen.
2015-02-27
Osayamba kapena kumalizila ndi chilumikazitsa.
71.
May not start or end with a dot, or contain the sequence "..".
2015-02-27
Osayamba kapena kumalizitsa ndi mpumulo, kapena mupimulo yotsatizana "..".
72.
You are running in debugging mode. Do not use a valuable password!
2015-02-27
Mukugwilitsa ntchito gawo lokhonzela ndi ku chotsa mavuta. Musagwilitse ntchito liwu lanu lachinsisi!
73.
Passwords do not match
2015-02-27
Mawu achinsisi akusiyana
74.
Short password
2015-02-27
Liwu lachinsisi lafupika
75.
Weak password
2015-02-27
Liwu lachinsisi lofooka
76.
Fair password
2015-02-27
Liwu lachinsisi labolako
77.
Good password
2015-02-27
Liwu la chinsisi labwino