Translations by Herald Luwizghie

Herald Luwizghie has submitted the following strings to this translation. Contributions are visually coded: currently used translations, unreviewed suggestions, rejected suggestions.

150 of 88 results
1.
Restart to Continue
2015-02-26
Yatsaninso kuti mupitilize
4.
Install
2015-02-26
Khazikitsani
5.
Install (OEM mode, for manufacturers only)
2015-02-26
Khazikitsani (gawo la OEM , la mafakitale okha)
6.
You are installing in system manufacturer mode. Please enter a unique name for this batch of systems. This name will be saved on the installed system and can be used to help with bug reports.
2015-02-26
Mukukhazikitsa makina awa mugawo la ku fakitale. Chonde lowetsani dzina lenileni la batch la makina awa. Dzinali lidza sungidwa mu sisitimu yo khazikidwa yi ndipo lidza thandiza popeleka malipoti ama vuto ena.
7.
You can try ${RELEASE} without making any changes to your computer, directly from this ${MEDIUM}.
2015-02-26
Mutha kuyesa ${RELEASE} popanda kusintha chilichonse muKomputa yanu podzela ku ${MEDIUM}
8.
Or if you're ready, you can install ${RELEASE} alongside (or instead of) your current operating system. This shouldn't take too long.
2015-02-27
Kapena ngati mwakhonzeka, mutha kukhazikitsa ${RELEASE} limodzi (kapena m'malo mwa) Operating system yomwe ilimo. Zimenezi sizikuyenela kutenga nthawi.
9.
Try ${RELEASE}
2015-02-27
Yesani ${RELEASE}
10.
Install ${RELEASE}
2015-02-27
Khazikitsani ${RELEASE}
11.
You may wish to read the release notes or update this installer.
2015-02-27
Muthakufuna kuwelenga izi release notes or update this installer
12.
You may wish to read the release notes.
2015-02-27
Muthakufuna kuwelenga izi release notes
13.
You may wish to update this installer.
2015-02-27
Muthakufuna ku update this installer
17.
Where are you?
2015-02-27
Mulikuti?
18.
Keyboard layout
2015-02-27
Kayalana kwa makiyi.
19.
Choose your keyboard layout:
2015-02-27
Sankhani kuyalana kwa makiyi.
20.
Type here to test your keyboard
2015-02-27
Lembani apa kuti muyese makiyi
21.
Detect Keyboard Layout
2015-02-27
Peza kayalidwe ka makiyi
22.
Detect Keyboard Layout...
2015-02-27
Peza kayalidwe ka makiyi...
23.
Please press one of the following keys:
2015-02-27
Chonde sindikizani limodzi mwa makiyi awa:
24.
Is the following key present on your keyboard?
2015-02-27
Kodi kiyi iyi ilipipo pa keyboard panu?
25.
Who are you?
2015-02-27
Ndiwe ndani?
27.
Your name:
2015-02-27
Dzina lanu:
28.
Your name
2015-02-27
Dzina lanu
29.
Pick a username:
2015-02-27
Sankhani dzina lomwe mudzigwilitsa ntchito
30.
Username
2015-02-27
Dzina lomwe mudzigwilitsa ntchito
31.
Choose a password:
2015-02-27
Sankhani liwu lachinsisi
32.
Password
2015-02-27
Liwu la Chinsinsi
33.
Confirm password
2015-02-27
Tsimikizani liwu lachinsinsi
34.
Confirm your password:
2015-02-27
Tsimikizanu liwu lanu lachinsisi
35.
Your computer's name:
2015-02-27
Dzina la kompyuta yanu
36.
The name it uses when it talks to other computers.
2015-02-27
Dzina limene idzagwilitse ntchitopoyankhula ndi zinzake.
37.
You are running in debugging mode. Do not use a valuable password!
2015-02-27
Mukugwilitsa ntchito gawo lokhonzela ndi ku chotsa mavuta. Musagwilitse ntchito liwu lanu lachinsisi!
38.
Passwords do not match
2015-02-27
Mawu achinsisi akusiyana
39.
Short password
2015-02-27
Liwu lachinsisi lafupika
40.
Weak password
2015-02-27
Liwu lachinsisi lofooka
41.
Fair password
2015-02-27
Liwu lachinsisi labolako
42.
Good password
2015-02-27
Liwu la chinsisi labwino
43.
Strong password
2015-03-04
Liwu la chinsisi lodalilika
44.
Log in automatically
2015-03-04
Lowani opanda mafunso
45.
Require my password to log in
2015-03-04
Funsa liwu la chinsisi polowa.
46.
Encrypt my home folder
2015-03-04
Kuika chinsisi pa folda yanga
50.
Installation type
2015-03-04
Ntundu waka khazikitsidwe
51.
Files (${SIZE})
2015-03-04
Mafailo (${SIZE})
52.
Prepare partitions
2015-03-04
Khonzekeletsani magawo
53.
_Install Now[ action ]
2015-03-04
_Khazikitsani Tsopano
54.
Quit the installation?
2015-03-04
Muimitse kukhazikitsa?
55.
Do you really want to quit the installation now?
2015-03-04
Mukufunutsitsadi kuimitsa kukhazikitsa uku pompano?
56.
Bootloader install failed
2015-03-04
Bootloader kukhazikitsa kwalepheleka
57.
Sorry, an error occurred and it was not possible to install the bootloader at the specified location.
2015-03-04
Pepani, papezeka vuto ndipo sizitheka kukhazikitsa bootloader pamalo omwemwa sankha
58.
Choose a different device to install the bootloader on:
2015-03-04
Sankhani makina kapena malo ena oti mukhazikitsile bootloader:
59.
Continue without a bootloader.
2015-03-04
Pitilizani popanda bootloader.